Salimo 30:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa mkwiyo wa Mulungu sukhalitsa pa munthu,+Koma kukoma mtima kwake ndi kwa moyo wonse.+Usiku kumakhala kulira,+ koma m’mawa kumakhala kufuula ndi chisangalalo.+ Salimo 103:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye sadzakhalira kutiimba mlandu nthawi zonse chifukwa cha zolakwa zathu,+Kapena kutisungira mkwiyo mpaka kalekale.+ Mika 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu+ amene amakhululukira zolakwa+ ndi machimo a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale, pakuti kusonyeza kukoma mtima kosatha kumakusangalatsani.+
5 Chifukwa mkwiyo wa Mulungu sukhalitsa pa munthu,+Koma kukoma mtima kwake ndi kwa moyo wonse.+Usiku kumakhala kulira,+ koma m’mawa kumakhala kufuula ndi chisangalalo.+
9 Iye sadzakhalira kutiimba mlandu nthawi zonse chifukwa cha zolakwa zathu,+Kapena kutisungira mkwiyo mpaka kalekale.+
18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu+ amene amakhululukira zolakwa+ ndi machimo a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale, pakuti kusonyeza kukoma mtima kosatha kumakusangalatsani.+