Yeremiya 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zimene Yehova wanena kwa anthu a ku Yuda ndi ku Yerusalemu ndi izi: “Limani minda panthaka yabwino, ndipo musabzale mbewu pakati pa minga.+
3 Zimene Yehova wanena kwa anthu a ku Yuda ndi ku Yerusalemu ndi izi: “Limani minda panthaka yabwino, ndipo musabzale mbewu pakati pa minga.+