Salimo 103:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye sadzakhalira kutiimba mlandu nthawi zonse chifukwa cha zolakwa zathu,+Kapena kutisungira mkwiyo mpaka kalekale.+ Yesaya 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu anthu anga amene mwapunthidwa ngati mbewu, ndi iwe mwana wa pamalo anga opunthira mbewu,+ zimene ndamva kwa Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, n’zimene ndakuuzani anthu inu. Mika 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu+ amene amakhululukira zolakwa+ ndi machimo a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale, pakuti kusonyeza kukoma mtima kosatha kumakusangalatsani.+ 1 Akorinto 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti m’chilamulo cha Mose muli mawu akuti: “Usamange ng’ombe pakamwa pamene ikupuntha mbewu.”+ Kodi ndi ng’ombe zimene Mulungu akusamalira?
9 Iye sadzakhalira kutiimba mlandu nthawi zonse chifukwa cha zolakwa zathu,+Kapena kutisungira mkwiyo mpaka kalekale.+
10 Inu anthu anga amene mwapunthidwa ngati mbewu, ndi iwe mwana wa pamalo anga opunthira mbewu,+ zimene ndamva kwa Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, n’zimene ndakuuzani anthu inu.
18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu+ amene amakhululukira zolakwa+ ndi machimo a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale, pakuti kusonyeza kukoma mtima kosatha kumakusangalatsani.+
9 Pakuti m’chilamulo cha Mose muli mawu akuti: “Usamange ng’ombe pakamwa pamene ikupuntha mbewu.”+ Kodi ndi ng’ombe zimene Mulungu akusamalira?