Levitiko 26:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Koma ngakhale kuti padzachitika zonsezi, pamene iwo akukhala m’dziko la adani awo, sindidzawakana+ kapena kunyansidwa nawo+ moti n’kuwafafaniziratu, kuphwanya pangano langa+ ndi iwo, chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wawo. Yesaya 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 M’tsiku limenelo, otsala a Isiraeli+ ndi opulumuka a nyumba ya Yakobo sadzadaliranso yemwe akuwamenya,+ koma ndi mtima wonse adzadalira Yehova, Woyera wa Isiraeli.+
44 Koma ngakhale kuti padzachitika zonsezi, pamene iwo akukhala m’dziko la adani awo, sindidzawakana+ kapena kunyansidwa nawo+ moti n’kuwafafaniziratu, kuphwanya pangano langa+ ndi iwo, chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wawo.
20 M’tsiku limenelo, otsala a Isiraeli+ ndi opulumuka a nyumba ya Yakobo sadzadaliranso yemwe akuwamenya,+ koma ndi mtima wonse adzadalira Yehova, Woyera wa Isiraeli.+