Yesaya 51:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zinthu ziwiri zidzakugwera.+ Kodi adzakumvera chisoni ndani?+ Udzalandidwa katundu ndi kuphwanyidwa, ndiponso udzakumana ndi njala ndi lupanga.+ Kodi adzakutonthoza ndani?+ Maliro 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Njira zopita ku Ziyoni zikulira, chifukwa palibe amene akupita kuchikondwerero.+Zipata zake zonse zasiyidwa.+ Ansembe+ ake akuusa moyo.*Anamwali ake agwidwa ndi chisoni,+ ndipo iyeyo akumva kuwawa mumtima.
19 Zinthu ziwiri zidzakugwera.+ Kodi adzakumvera chisoni ndani?+ Udzalandidwa katundu ndi kuphwanyidwa, ndiponso udzakumana ndi njala ndi lupanga.+ Kodi adzakutonthoza ndani?+
4 Njira zopita ku Ziyoni zikulira, chifukwa palibe amene akupita kuchikondwerero.+Zipata zake zonse zasiyidwa.+ Ansembe+ ake akuusa moyo.*Anamwali ake agwidwa ndi chisoni,+ ndipo iyeyo akumva kuwawa mumtima.