Yesaya 29:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Khamu la anthu achilendo lidzasanduka fumbi losalala,+ ndipo khamu la olamulira ankhanza+ lidzakhala ngati mankhusu amene akuuluzika.+ Zimenezi zidzachitika mwadzidzidzi, mosayembekezereka.+
5 Khamu la anthu achilendo lidzasanduka fumbi losalala,+ ndipo khamu la olamulira ankhanza+ lidzakhala ngati mankhusu amene akuuluzika.+ Zimenezi zidzachitika mwadzidzidzi, mosayembekezereka.+