Mateyu 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo Afarisi anachoka ndi kukapangana kuti am’kole m’mawu ake.+ Luka 11:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Anali kuyembekezera+ kumva mawu oti amutape nawo m’kamwa.+