Yesaya 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nthaka ndidzaibwezera zoipa zake,+ ndipo anthu oipa ndidzawabwezera zolakwa zawo. Kunyada kwa anthu odzikuza ndidzakuthetsa, ndipo ndidzatsitsa olamulira ankhanza ndi odzikweza.+ Yeremiya 48:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Tamva za kunyada kwa Mowabu.+ Iye ndi wodzikuza kwambiri. Tamva za kudzikweza kwake, kunyada kwake, kudzikuza kwake ndi kudzitukumula kwa mtima wake.”+ Ezekieli 28:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wachulukitsa chuma chako+ chifukwa chakuti uli ndi nzeru zochuluka+ komanso umachita malonda.+ Chotero mtima wako wayamba kudzikuza chifukwa cha chuma chakocho.”’+
11 Nthaka ndidzaibwezera zoipa zake,+ ndipo anthu oipa ndidzawabwezera zolakwa zawo. Kunyada kwa anthu odzikuza ndidzakuthetsa, ndipo ndidzatsitsa olamulira ankhanza ndi odzikweza.+
29 “Tamva za kunyada kwa Mowabu.+ Iye ndi wodzikuza kwambiri. Tamva za kudzikweza kwake, kunyada kwake, kudzikuza kwake ndi kudzitukumula kwa mtima wake.”+
5 Wachulukitsa chuma chako+ chifukwa chakuti uli ndi nzeru zochuluka+ komanso umachita malonda.+ Chotero mtima wako wayamba kudzikuza chifukwa cha chuma chakocho.”’+