Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Nyamukani, inu Yehova, mu mkwiyo wanu.+

      Imirirani ndi kukhaulitsa amene andisonyeza mkwiyo ndi kundichitira zoipa.+

      Dzukani ndi kundithandiza,+ pakuti mwalamula kuti chiweruzo chiperekedwe.+

  • Mika 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Tamverani! Yehova akuchoka pamalo ake,+ ndipo atsika ndi kupondaponda m’malo okwezeka a padziko lapansi.+

  • Aheberi 12:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Pa nthawiyo, mawu ake anagwedeza dziko lapansi,+ koma tsopano walonjeza kuti: “Ndidzagwedezanso kumwamba, osati dziko lapansi lokhali.”+

  • 2 Petulo 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Komabe, tsiku la Yehova+ lidzafika ngati mbala,+ pamene kumwamba kudzachoka+ ndi mkokomo waukulu,+ koma zinthu zimene zimapanga kumwamba ndi dziko lapansi zidzatentha kwambiri n’kusungunuka,+ ndipo dziko lapansi+ ndi ntchito zake zidzaonekera poyera.+

  • Chivumbulutso 16:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Pamenepo kunachitika mphezi, kunamveka mawu, ndipo kunagunda mabingu. Kunachitanso chivomezi chachikulu+ chimene sichinachitikepo chikhalire anthu padziko lapansi,+ chivomezi+ champhamvu kwambiri, chachikulu zedi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena