Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Dziko lawo ladzaza ndi milungu yopanda phindu.+ Iwo amagwadira ntchito ya manja awo. Amagwadira chinthu chimene zala zawo zapanga.+

  • Yesaya 30:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Zophimbira mafano anu ogoba asiliva ndi zokutira zifaniziro zanu zopangidwa ndi golide+ wosungunula,+ mudzaziona kuti ndi zonyansa+ ndipo mudzazitaya.+ Monga mkazi amene akusamba yemwe amataya monyansidwa kansalu kake, mudzanena kuti: “Nyansi zimenezi!”+

  • Yesaya 31:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pakuti m’tsiku limenelo, aliyense wa inu adzataya milungu yake yasiliva yachabechabe, ndi milungu yake yagolide yopanda phindu,+ imene manja anu akupangirani n’kukuchimwitsani nayo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena