Genesis 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako, Yehova Mulungu anaumba munthu kuchokera kufumbi lapansi,+ ndipo anauzira mpweya wa moyo+ m’mphuno mwake, munthuyo n’kukhala wamoyo.+ Yobu 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamene mpweya wanga udakali wonse mwa ine,Ndiponso pamene mzimu wa Mulungu udakali m’mphuno mwanga,+
7 Kenako, Yehova Mulungu anaumba munthu kuchokera kufumbi lapansi,+ ndipo anauzira mpweya wa moyo+ m’mphuno mwake, munthuyo n’kukhala wamoyo.+
3 Pamene mpweya wanga udakali wonse mwa ine,Ndiponso pamene mzimu wa Mulungu udakali m’mphuno mwanga,+