Yesaya 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho Yehova adzachititsa zipere+ m’mutu mwa ana aakazi a Ziyoni, ndipo Yehova adzayeretsa pamutu pawo.+ Yeremiya 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndidzathetsa phokoso lachikondwerero ndi phokoso lakusangalala m’malowo.+ Ndidzathetsanso mawu osangalala a mkwati ndi a mkwatibwi.+ Simudzamvekanso kupera kwa mphero+ ndipo simudzaonekanso kuwala kwa nyale.+
17 Choncho Yehova adzachititsa zipere+ m’mutu mwa ana aakazi a Ziyoni, ndipo Yehova adzayeretsa pamutu pawo.+
10 Ndidzathetsa phokoso lachikondwerero ndi phokoso lakusangalala m’malowo.+ Ndidzathetsanso mawu osangalala a mkwati ndi a mkwatibwi.+ Simudzamvekanso kupera kwa mphero+ ndipo simudzaonekanso kuwala kwa nyale.+