Ezekieli 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Uza anthu amene akupaka laimuwo kuti khomalo lidzagwa. Kudzagwa mvula yambiri imene madzi ake adzasefukira. Kudzagwa matalala ndipo mphepo yamkuntho idzang’amba khomalo.+
11 “Uza anthu amene akupaka laimuwo kuti khomalo lidzagwa. Kudzagwa mvula yambiri imene madzi ake adzasefukira. Kudzagwa matalala ndipo mphepo yamkuntho idzang’amba khomalo.+