Yesaya 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti nyenyezi zakumwamba ndi magulu a nyenyezi a Kesili+ sizidzawala. Dzuwa lidzachita mdima potuluka, ndipo mwezi sudzaonetsa kuwala kwake. Obadiya 4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ngakhale malo ako atakhala pamwamba ngati a chiwombankhanga, kapena ngakhale utamanga chisa chako pakati pa nyenyezi, ine ndidzakugwetsa kuchokera pamenepo,”+ watero Yehova. Obadiya 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kodi pa tsiku limenelo sindidzawononga anthu anzeru mu Edomu?”+ watero Yehova. “Ndiponso kodi sindidzawononga anthu ozindikira a m’dera lamapiri la Esau?
10 Pakuti nyenyezi zakumwamba ndi magulu a nyenyezi a Kesili+ sizidzawala. Dzuwa lidzachita mdima potuluka, ndipo mwezi sudzaonetsa kuwala kwake.
4 Ngakhale malo ako atakhala pamwamba ngati a chiwombankhanga, kapena ngakhale utamanga chisa chako pakati pa nyenyezi, ine ndidzakugwetsa kuchokera pamenepo,”+ watero Yehova.
8 Kodi pa tsiku limenelo sindidzawononga anthu anzeru mu Edomu?”+ watero Yehova. “Ndiponso kodi sindidzawononga anthu ozindikira a m’dera lamapiri la Esau?