Levitiko 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotero asamaperekenso nsembe zawo ku ziwanda zooneka ngati mbuzi*+ zimene akuchita nazo chiwerewere.+ Limeneli likhale lamulo kwa inu mpaka kalekale, m’mibadwo yanu yonse.”’ 2 Mbiri 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye anadziikira ansembe m’malo okwezeka+ kuti azitumikira ziwanda zooneka ngati mbuzi*+ ndi mafano a ana a ng’ombe amene iye anapanga.+
7 Chotero asamaperekenso nsembe zawo ku ziwanda zooneka ngati mbuzi*+ zimene akuchita nazo chiwerewere.+ Limeneli likhale lamulo kwa inu mpaka kalekale, m’mibadwo yanu yonse.”’
15 Iye anadziikira ansembe m’malo okwezeka+ kuti azitumikira ziwanda zooneka ngati mbuzi*+ ndi mafano a ana a ng’ombe amene iye anapanga.+