Yesaya 34:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mbalame zotchedwa vuwo ndi nungu zidzakhala kumeneko. Komanso akadzidzi a makutu ataliatali ndi akhwangwala azidzakhala kumeneko.+ Iye adzatambasulira dzikolo chingwe choyezera+ malo opanda kanthu, ndiponso miyala yoyezera kuwongoka kwa chinthu.
11 Mbalame zotchedwa vuwo ndi nungu zidzakhala kumeneko. Komanso akadzidzi a makutu ataliatali ndi akhwangwala azidzakhala kumeneko.+ Iye adzatambasulira dzikolo chingwe choyezera+ malo opanda kanthu, ndiponso miyala yoyezera kuwongoka kwa chinthu.