Genesis 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Udzalowetsenso m’chingalawacho chamoyo chilichonse cha mtundu uliwonse.+ Udzazilowetse ziwiriziwiri, champhongo ndi chachikazi, kuti zidzasungike zamoyo limodzi nawe.+
19 Udzalowetsenso m’chingalawacho chamoyo chilichonse cha mtundu uliwonse.+ Udzazilowetse ziwiriziwiri, champhongo ndi chachikazi, kuti zidzasungike zamoyo limodzi nawe.+