2 Mafumu 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iwe wanena kuti (koma ndi mawu a pakamwa chabe), ‘Ine ndili ndi nzeru+ ndi mphamvu zofunika pankhondo.’ Kodi ukudalira ndani popandukira+ ine?
20 Iwe wanena kuti (koma ndi mawu a pakamwa chabe), ‘Ine ndili ndi nzeru+ ndi mphamvu zofunika pankhondo.’ Kodi ukudalira ndani popandukira+ ine?