2 Mbiri 32:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Hezekiyatu+ akungokunyengererani+ kuti mufe ndi njala ndi ludzu pokuuzani kuti: “Yehova Mulungu wathu atipulumutsa m’manja mwa mfumu ya Asuri.”+ Yesaya 37:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Amuna inu mukamuuze Hezekiya mfumu ya Yuda kuti, ‘Usalole Mulungu wako amene ukumudalira kuti akunamize,+ ponena kuti: “Yerusalemu saperekedwa m’manja mwa mfumu ya Asuri.”+
11 Hezekiyatu+ akungokunyengererani+ kuti mufe ndi njala ndi ludzu pokuuzani kuti: “Yehova Mulungu wathu atipulumutsa m’manja mwa mfumu ya Asuri.”+
10 “Amuna inu mukamuuze Hezekiya mfumu ya Yuda kuti, ‘Usalole Mulungu wako amene ukumudalira kuti akunamize,+ ponena kuti: “Yerusalemu saperekedwa m’manja mwa mfumu ya Asuri.”+