1 Mafumu 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ayuda ndi Aisiraeli anachuluka kwambiri.+ Kuchuluka kwake anali ngati mchenga wa m’mphepete mwa nyanja, ndipo anali kudya, kumwa, ndi kusangalala.+ Mika 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Aliyense adzakhala pansi pa mtengo wake wa mpesa ndi mtengo wake wa mkuyu+ ndipo sipadzakhala wowaopsa,+ pakuti pakamwa pa Yehova wa makamu panena zimenezi.+ Zekariya 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Pa tsiku limenelo mudzaitanizana, aliyense atakhala pansi pa mtengo wake wa mpesa ndiponso wa mkuyu,’+ watero Yehova wa makamu.”
20 Ayuda ndi Aisiraeli anachuluka kwambiri.+ Kuchuluka kwake anali ngati mchenga wa m’mphepete mwa nyanja, ndipo anali kudya, kumwa, ndi kusangalala.+
4 Aliyense adzakhala pansi pa mtengo wake wa mpesa ndi mtengo wake wa mkuyu+ ndipo sipadzakhala wowaopsa,+ pakuti pakamwa pa Yehova wa makamu panena zimenezi.+
10 “‘Pa tsiku limenelo mudzaitanizana, aliyense atakhala pansi pa mtengo wake wa mpesa ndiponso wa mkuyu,’+ watero Yehova wa makamu.”