Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 58:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Oipa akhala opotoka maganizo kuyambira ali m’mimba.+

      Iwo asochera kuyambira ali m’mimba,

      Ndipo amalankhula zabodza.+

  • Yeremiya 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Yehova wanena kuti: “Kodi makolo anu anandipeza ndi chiyani chosalungama+ kuti akhale patali ndi ine?+ Anandipeza ndi chiyani kuti ayambe kutsatira fano lopanda pake+ iwonso n’kukhala anthu opanda pake?+

  • Yeremiya 15:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “‘Iwe wandisiya,’+ watero Yehova. ‘Ukundifulatira ndi kundichokera.+ Choncho nditambasula dzanja langa kuti ndikukanthe ndi kukuwononga.+ Ndatopa nako kukumvera chisoni.+

  • Aroma 8:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 chifukwa kuika maganizo pa zinthu za thupi ndiko udani+ ndi Mulungu, popeza thupi siligonjera+ chilamulo cha Mulungu, ndipotu kunena zoona, silingachigonjere.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena