Salimo 48:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kumeneko iwo anayamba kunjenjemera,+Anamva zopweteka ngati za mkazi amene akubereka.+ Salimo 127:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 127 Yehova akapanda kumanga nyumba,+Omanga nyumbayo amagwira ntchito pachabe.+Yehova akapanda kulondera mzinda,+Alonda amakhala maso pachabe.+
127 Yehova akapanda kumanga nyumba,+Omanga nyumbayo amagwira ntchito pachabe.+Yehova akapanda kulondera mzinda,+Alonda amakhala maso pachabe.+