-
Levitiko 25:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Musakolole mbewu zomera zokha zochokera pa zimene munakolola chaka chapita, ndipo musakololenso mphesa za m’mitengo yanu yosadulirayo. M’chaka chimenecho dziko lizipumula pa zonse.
-