2 Mafumu 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndithu ndiwonjezera zaka 15 pa masiku ako, ndipo ndidzalanditsa+ iweyo ndi mzindawu m’manja mwa mfumu ya Asuri. Ndidzateteza mzinda uno chifukwa cha ine mwini ndiponso chifukwa cha Davide mtumiki wanga.”’”+ Salimo 91:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndidzamukhutiritsa ndi masiku ambiri,+Ndipo ndidzamuonetsa chipulumutso changa.”+
6 Ndithu ndiwonjezera zaka 15 pa masiku ako, ndipo ndidzalanditsa+ iweyo ndi mzindawu m’manja mwa mfumu ya Asuri. Ndidzateteza mzinda uno chifukwa cha ine mwini ndiponso chifukwa cha Davide mtumiki wanga.”’”+