2 Mafumu 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo mneneri Yesaya anayamba kufuulira Yehova, ndipo iye anachititsa mthunzi umene unali utapita kale kutsogolo kuti ubwerere m’mbuyo pang’onopang’ono pamasitepe a Ahazi. Mthunziwo unabwerera m’mbuyo masitepe 10.+
11 Pamenepo mneneri Yesaya anayamba kufuulira Yehova, ndipo iye anachititsa mthunzi umene unali utapita kale kutsogolo kuti ubwerere m’mbuyo pang’onopang’ono pamasitepe a Ahazi. Mthunziwo unabwerera m’mbuyo masitepe 10.+