Yobu 33:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Iye wandiwombola kuti ndisapite kudzenje,+Ndipo moyo wanga udzaona kuwala.’ Salimo 71:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chifukwa chakuti mwandionetsa masautso ndi masoka ambiri,+Nditsitsimutseni.+Nditulutseninso m’madzi akuya, pansi pa nthaka.+
20 Chifukwa chakuti mwandionetsa masautso ndi masoka ambiri,+Nditsitsimutseni.+Nditulutseninso m’madzi akuya, pansi pa nthaka.+