Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 29:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pa chifukwa chimenechi, makolo athu anaphedwa ndi lupanga+ ndipo ana athu aamuna ndi aakazi ndiponso akazi athu anapita ku ukapolo.+

  • Yeremiya 11:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Yehova wa makamu wanena kuti: “Tsopano ndikuwapatsa chilango. Anyamata adzafa ndi lupanga.+ Ana awo aamuna ndi aakazi adzafa ndi njala yaikulu.+

  • Maliro 2:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Anyamata ndi amuna okalamba+ agona pansi m’misewu.+

      Anamwali anga ndi anyamata anga aphedwa ndi lupanga.+

      Mwapha anthu pa tsiku la mkwiyo+ wanu. Onsewo mwawaphadi+ mopanda chisoni.+

  • Amosi 9:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Anthu anga onse ochimwa adzaphedwa ndi lupanga.+ Iwo amanena kuti: “Tsoka silitiyandikira kapena kutigwera.”’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena