Salimo 79:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Musatiimbe mlandu chifukwa cha zolakwa za makolo athu.+Fulumirani! Tisonyezeni chifundo chanu,+Chifukwa tasautsika koopsa.+ Salimo 103:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Monga mmene bambo amasonyezera chifundo kwa ana ake,+Yehova wasonyezanso chifundo kwa onse omuopa.+
8 Musatiimbe mlandu chifukwa cha zolakwa za makolo athu.+Fulumirani! Tisonyezeni chifundo chanu,+Chifukwa tasautsika koopsa.+
13 Monga mmene bambo amasonyezera chifundo kwa ana ake,+Yehova wasonyezanso chifundo kwa onse omuopa.+