Yesaya 55:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 ndi mmenenso adzakhalire mawu otuluka pakamwa panga.+ Sadzabwerera kwa ine popanda kukwaniritsa cholinga chake,+ koma adzachitadi zimene ine ndikufuna+ ndipo adzakwaniritsadi zimene ndinawatumizira.+ Tito 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kumene kwazikidwa pa chiyembekezo cha moyo wosatha,+ chomwe Mulungu amene sanganame,+ analonjeza kalekale.+
11 ndi mmenenso adzakhalire mawu otuluka pakamwa panga.+ Sadzabwerera kwa ine popanda kukwaniritsa cholinga chake,+ koma adzachitadi zimene ine ndikufuna+ ndipo adzakwaniritsadi zimene ndinawatumizira.+
2 kumene kwazikidwa pa chiyembekezo cha moyo wosatha,+ chomwe Mulungu amene sanganame,+ analonjeza kalekale.+