Salimo 90:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwawawonongeratu,+ ndipo amangozimiririka ngati maloto.+M’mawa amakhala ngati msipu wobiriwira umene watsitsimuka.+ Salimo 103:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mphepo ikawomba limafa,+Ndipo pamalo amene linali sipadziwikanso,+ Salimo 104:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mukaphimba nkhope yanu, zimasokonezeka.+Mukachotsa mzimu wawo, zimafa,+Ndipo zimabwerera kufumbi.+
5 Mwawawonongeratu,+ ndipo amangozimiririka ngati maloto.+M’mawa amakhala ngati msipu wobiriwira umene watsitsimuka.+
29 Mukaphimba nkhope yanu, zimasokonezeka.+Mukachotsa mzimu wawo, zimafa,+Ndipo zimabwerera kufumbi.+