Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 51:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Ndimvereni, inu odziwa chilungamo, inu amene muli ndi lamulo langa mumtima mwanu.+ Musaope chitonzo cha anthu ndipo musachite mantha chifukwa cha mawu awo onyoza.+

  • Yohane 12:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Usaope mwana wamkazi wa Ziyoni. Taona! Mfumu yako ikubwera.+ Ikubwera itakwera bulu wamng’ono wamphongo.”+

  • Afilipi 1:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Komanso simukuchita mantha m’njira iliyonse ndi okutsutsani.+ Kwa iwo, chimenechi ndi chizindikiro chakuti adzawonongedwa, koma kwa inu, ndi chizindikiro cha chipulumutso.+ Chizindikiro chimenechi n’chochokera kwa Mulungu.

  • 1 Petulo 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma ngakhale mutavutika chifukwa cha chilungamo, mudzakhalabe odala.+ Musaope zimene iwo amaopa,+ ndipo musade nazo nkhawa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena