Yesaya 41:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zilumba+ zinaona n’kuyamba kuopa. Malekezero a dziko lapansi anayamba kunjenjemera.+ Mitundu ya anthu inasonkhana pamodzi n’kumangobwerabe.
5 Zilumba+ zinaona n’kuyamba kuopa. Malekezero a dziko lapansi anayamba kunjenjemera.+ Mitundu ya anthu inasonkhana pamodzi n’kumangobwerabe.