Ezekieli 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthu ako ndidzawabalalitsira ku mitundu ina ya anthu ndipo ndidzawamwaza m’mayiko osiyanasiyana.+ Komanso ndidzachotsa zodetsa zako mwa iwe.+ Ezekieli 36:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ine ndidzakuwazani madzi oyera ndipo mudzakhala oyera. Ndidzakuyeretsani+ pokuchotserani zonyansa zanu zonse+ ndi mafano anu onse onyansa.+
15 Anthu ako ndidzawabalalitsira ku mitundu ina ya anthu ndipo ndidzawamwaza m’mayiko osiyanasiyana.+ Komanso ndidzachotsa zodetsa zako mwa iwe.+
25 Ine ndidzakuwazani madzi oyera ndipo mudzakhala oyera. Ndidzakuyeretsani+ pokuchotserani zonyansa zanu zonse+ ndi mafano anu onse onyansa.+