Deuteronomo 33:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mulungu wakale lomwe ndiwo malo ako obisalamo,+Ndipo iwe uli m’manja amene adzakhalapo mpaka kalekale.+Adzapitikitsa mdani pamaso pako,+Ndipo adzanena kuti, ‘Awononge!’+ Salimo 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova adzapatsa anthu ake mphamvu.+Yehova adzadalitsa anthu ake ndi mtendere.+ Zekariya 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ine Yehova ndidzawachititsa kukhala amphamvu+ ndipo zochita zawo zidzalemekeza dzina langa,’+ watero Yehova.”
27 Mulungu wakale lomwe ndiwo malo ako obisalamo,+Ndipo iwe uli m’manja amene adzakhalapo mpaka kalekale.+Adzapitikitsa mdani pamaso pako,+Ndipo adzanena kuti, ‘Awononge!’+
12 Ine Yehova ndidzawachititsa kukhala amphamvu+ ndipo zochita zawo zidzalemekeza dzina langa,’+ watero Yehova.”