Salimo 63:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndakulondolani kulikonse,+Dzanja lanu lamanja landigwira mwamphamvu.+