Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 43:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Inu ndinu mboni zanga,”+ akutero Yehova. “Ndinu mtumiki wanga amene ndakusankhani+ kuti mundidziwe+ ndi kundikhulupirira,+ komanso kuti mumvetse kuti ine sindinasinthe.+ Ine ndisanakhaleko kunalibe Mulungu amene anapangidwa,+ ndipo pambuyo panga palibenso wina.+

  • Yesaya 44:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndani ali ngati ine?+ Ayankhe molimba mtima kuti apereke umboni wake kwa ine.+ Monga momwe ine ndachitira kuyambira nthawi imene ndinakhazikitsa anthu akalekale,+ iwo anene zinthu zimene zichitike posachedwa ndi zimene zidzachitike m’tsogolo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena