Mateyu 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Taonani mtumiki wanga+ amene ndamusankha, wokondedwa wanga,+ amene moyo wanga ukukondwera naye. Ndidzaika mzimu wanga pa iye,+ ndipo adzasonyeza bwinobwino chilungamo chenicheni kwa anthu a mitundu ina. Aroma 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 kuti mitundu ina+ ipereke ulemerero kwa Mulungu chifukwa cha chifundo+ chake, monga mmene Malemba amanenera kuti: “N’chifukwa chake ndidzakuvomerezani poyera pakati pa mitundu. Ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.”+
18 “Taonani mtumiki wanga+ amene ndamusankha, wokondedwa wanga,+ amene moyo wanga ukukondwera naye. Ndidzaika mzimu wanga pa iye,+ ndipo adzasonyeza bwinobwino chilungamo chenicheni kwa anthu a mitundu ina.
9 kuti mitundu ina+ ipereke ulemerero kwa Mulungu chifukwa cha chifundo+ chake, monga mmene Malemba amanenera kuti: “N’chifukwa chake ndidzakuvomerezani poyera pakati pa mitundu. Ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.”+