Nehemiya 9:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Mafumu athu, akalonga athu, ansembe athu ndi makolo athu+ sanatsatire chilamulo chanu+ ndipo sanamvere malamulo anu+ kapena zikumbutso zanu zowachenjeza.+ Danieli 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Inu Yehova, manyazi aphimba nkhope zathu, za mafumu athu, akalonga athu ndi makolo athu chifukwa takuchimwirani.+
34 Mafumu athu, akalonga athu, ansembe athu ndi makolo athu+ sanatsatire chilamulo chanu+ ndipo sanamvere malamulo anu+ kapena zikumbutso zanu zowachenjeza.+
8 “Inu Yehova, manyazi aphimba nkhope zathu, za mafumu athu, akalonga athu ndi makolo athu chifukwa takuchimwirani.+