Salimo 91:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 91 Aliyense wokhala m’malo otetezeka+ a Wam’mwambamwamba+Adzakhala wosungika mumthunzi wa Wamphamvuyonse.+ Salimo 121:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova akukuyang’anira.+Yehova ndiye mthunzi wako+ kudzanja lako lamanja.+
91 Aliyense wokhala m’malo otetezeka+ a Wam’mwambamwamba+Adzakhala wosungika mumthunzi wa Wamphamvuyonse.+