Deuteronomo 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Koma khalani tcheru ndipo musamale moyo wanu,+ kuti musaiwale zinthu zimene maso anu anaona,+ ndi kuti mitima yanu isaiwale zinthu zimenezo masiku onse a moyo wanu.+ Ana anu ndi zidzukulu zanu muziwauza za zinthu zimenezo,+ Deuteronomo 29:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Yehova sanakupatseni mtima woti muthe kuzindikira, maso oti muthe kuona ndi makutu oti muthe kumva, kufikira lero.+ Salimo 106:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Makolo athu ku Iguputo,Sanasonyeze kuzindikira kulikonse ntchito zanu zodabwitsa.+Sanakumbukire kuchuluka kwa kukoma mtima kwanu kosatha,+Koma anapanduka panyanja, pafupi ndi Nyanja Yofiira.+
9 “Koma khalani tcheru ndipo musamale moyo wanu,+ kuti musaiwale zinthu zimene maso anu anaona,+ ndi kuti mitima yanu isaiwale zinthu zimenezo masiku onse a moyo wanu.+ Ana anu ndi zidzukulu zanu muziwauza za zinthu zimenezo,+
4 Koma Yehova sanakupatseni mtima woti muthe kuzindikira, maso oti muthe kuona ndi makutu oti muthe kumva, kufikira lero.+
7 Makolo athu ku Iguputo,Sanasonyeze kuzindikira kulikonse ntchito zanu zodabwitsa.+Sanakumbukire kuchuluka kwa kukoma mtima kwanu kosatha,+Koma anapanduka panyanja, pafupi ndi Nyanja Yofiira.+