Yeremiya 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova wanena kuti: “Kodi makolo anu anandipeza ndi chiyani chosalungama+ kuti akhale patali ndi ine?+ Anandipeza ndi chiyani kuti ayambe kutsatira fano lopanda pake+ iwonso n’kukhala anthu opanda pake?+ Mika 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu mapiri, imvani mlandu umene Yehova ali nawo pa anthu ake. Inu matanthwe okhazikika, tamverani. Mvetserani inu maziko a dziko lapansi,+ pakuti Yehova ali ndi mlandu ndi anthu ake. Iye azenga mlandu Aisiraeli, kuti:+
5 Yehova wanena kuti: “Kodi makolo anu anandipeza ndi chiyani chosalungama+ kuti akhale patali ndi ine?+ Anandipeza ndi chiyani kuti ayambe kutsatira fano lopanda pake+ iwonso n’kukhala anthu opanda pake?+
2 Inu mapiri, imvani mlandu umene Yehova ali nawo pa anthu ake. Inu matanthwe okhazikika, tamverani. Mvetserani inu maziko a dziko lapansi,+ pakuti Yehova ali ndi mlandu ndi anthu ake. Iye azenga mlandu Aisiraeli, kuti:+