Salimo 95:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Bwerani timuweramire ndi kumupembedza.+Tiyeni tigwade+ pamaso pa Yehova amene ndiye Wotipanga.+ Salimo 100:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Dziwani kuti Yehova ndi Mulungu.+Iye ndi amene anatipanga, sitinadzipange tokha.+Ndife anthu ake ndi nkhosa zimene akuweta.+ Yesaya 29:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 pakuti akaona ana ake pakati pake, ntchito ya manja anga,+ iwo adzayeretsa dzina langa.+ Adzayeretsadi Woyera wa Yakobo,+ ndipo adzalemekeza kwambiri Mulungu wa Isiraeli.+
3 Dziwani kuti Yehova ndi Mulungu.+Iye ndi amene anatipanga, sitinadzipange tokha.+Ndife anthu ake ndi nkhosa zimene akuweta.+
23 pakuti akaona ana ake pakati pake, ntchito ya manja anga,+ iwo adzayeretsa dzina langa.+ Adzayeretsadi Woyera wa Yakobo,+ ndipo adzalemekeza kwambiri Mulungu wa Isiraeli.+