Yobu 40:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Takokera chovala chako n’kuchimanga m’chiuno ngati mwamuna wamphamvu.+Ndikufuna ndikufunse mafunso ndipo iweyo undiyankhe.+ Luka 10:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma pofuna kudzionetsa kuti ndi wolungama, munthuyo anafunsa Yesu kuti: “Nanga mnzanga amene ndikuyenera kumukonda ndani kwenikweni?”+
7 “Takokera chovala chako n’kuchimanga m’chiuno ngati mwamuna wamphamvu.+Ndikufuna ndikufunse mafunso ndipo iweyo undiyankhe.+
29 Koma pofuna kudzionetsa kuti ndi wolungama, munthuyo anafunsa Yesu kuti: “Nanga mnzanga amene ndikuyenera kumukonda ndani kwenikweni?”+