Salimo 71:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kuyambira ndili m’mimba mwa mayi anga inu mwandithandiza.+Inu ndi amene munanditulutsa m’mimba mwa mayi anga.+Ndimatamanda inu nthawi zonse.+ Yesaya 49:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ndimvereni zilumba inu,+ ndipo mvetserani, inu mitundu ya anthu akutali.+ Yehova anandiitana+ ndili m’mimba.+ Ndili mkati mwa mayi anga, anatchula dzina langa.+ Yeremiya 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Ndisanakuumbe m’mimba,+ ndinakudziwa,+ ndipo usanatuluke m’mimbamo, ndinakusankha kuti uchite ntchito yopatulika.+ Ndinakusankha kuti ukhale mneneri ku mitundu ya anthu.”
6 Kuyambira ndili m’mimba mwa mayi anga inu mwandithandiza.+Inu ndi amene munanditulutsa m’mimba mwa mayi anga.+Ndimatamanda inu nthawi zonse.+
49 Ndimvereni zilumba inu,+ ndipo mvetserani, inu mitundu ya anthu akutali.+ Yehova anandiitana+ ndili m’mimba.+ Ndili mkati mwa mayi anga, anatchula dzina langa.+
5 “Ndisanakuumbe m’mimba,+ ndinakudziwa,+ ndipo usanatuluke m’mimbamo, ndinakusankha kuti uchite ntchito yopatulika.+ Ndinakusankha kuti ukhale mneneri ku mitundu ya anthu.”