Deuteronomo 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mukatero mkwiyo wa Yehova udzakuyakirani. Adzatseka kumwamba moti mvula sidzagwa+ ndipo nthaka sidzatulutsa zipatso zake. Pamenepo mudzafafanizika mwamsanga m’dziko labwinolo limene Yehova akukupatsani.+ Deuteronomo 28:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Thambo limene lili pamwamba pa mutu wako lidzakhala ngati mkuwa, ndipo nthaka yako idzakhala ngati chitsulo.+ Amosi 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “‘Ine ndinakumanani mvula kutatsala miyezi itatu kuti mukolole.+ Ndinagwetsa mvula pamzinda umodzi koma pamzinda wina sindinagwetsepo mvula. Mvula inagwa pamunda umodzi koma pamunda wina sindinagwetsepo mvula ndipo unauma.+
17 Mukatero mkwiyo wa Yehova udzakuyakirani. Adzatseka kumwamba moti mvula sidzagwa+ ndipo nthaka sidzatulutsa zipatso zake. Pamenepo mudzafafanizika mwamsanga m’dziko labwinolo limene Yehova akukupatsani.+
23 Thambo limene lili pamwamba pa mutu wako lidzakhala ngati mkuwa, ndipo nthaka yako idzakhala ngati chitsulo.+
7 “‘Ine ndinakumanani mvula kutatsala miyezi itatu kuti mukolole.+ Ndinagwetsa mvula pamzinda umodzi koma pamzinda wina sindinagwetsepo mvula. Mvula inagwa pamunda umodzi koma pamunda wina sindinagwetsepo mvula ndipo unauma.+