Luka 10:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Choncho anam’yandikira ndi kumanga mabala ake. Anathira mafuta ndi vinyo m’mabalamo.+ Kenako anam’kweza pachiweto chake n’kupita naye kunyumba ya alendo kumene anam’samalira.
34 Choncho anam’yandikira ndi kumanga mabala ake. Anathira mafuta ndi vinyo m’mabalamo.+ Kenako anam’kweza pachiweto chake n’kupita naye kunyumba ya alendo kumene anam’samalira.