Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 29:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Anthu inu ndinu opotoka maganizo kwabasi! Kodi woumba zinthu ndi dongo angafanane ndi dongolo?+ Kodi chinthu chochita kupangidwa chingamunene amene anachipanga, kuti: “Iye uja sanandipange”?+ Komanso kodi chinthu chochita kuumbidwa chingamunene amene anachiumba, kuti: “Iye uja sanasonyeze kuti ndi womvetsa zinthu”?+

  • Yeremiya 18:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “‘Anthu inu, kodi sindingathe kukuchitirani mofanana ndi mmene woumba mbiyayu anachitira, inu nyumba ya Isiraeli?’ watero Yehova. ‘Taonani! Mofanana ndi dongo limene lili m’manja mwa woumba mbiya, ndi mmene inunso mulili kwa ine, inu nyumba ya Isiraeli.+

  • Aroma 9:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Munthu iwe!+ Iweyo ndiwe ndani kuti uziyankhana ndi Mulungu?+ Kodi chinthu choumbidwa chinganene kwa munthu amene anachiumba kuti, “Unandipangiranji motere?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena