Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Esitere 8:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 M’zigawo zonse ndi m’mizinda yonse kumene mawu a mfumu ndi lamulo lake linafika, Ayuda anali kusangalala ndi kukondwera. Anachita phwando+ ndipo linali tsiku lachisangalalo. Anthu ambiri+ a m’dzikomo anayamba kudzitcha Ayuda+ chifukwa anali kuchita mantha kwambiri+ ndi Ayudawo.

  • Yesaya 14:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Anthu a mitundu ina adzawatenga n’kubwerera nawo kwawo ndipo nyumba ya Isiraeli idzatenga anthuwo kuti akhale awo m’dziko la Yehova, ndiponso kuti akhale antchito awo aamuna ndi aakazi.+ Iwo adzagwira+ anthu amene anawagwira n’kupita nawo kudziko lina ndipo azidzalamulira anthu amene anali kuwagwiritsa ntchito.+

  • Yesaya 60:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Ana a anthu okusautsa adzabwera kwa iwe atawerama.+ Onse amene anali kukuchitira chipongwe adzagwada pamapazi ako,+ ndipo adzakutcha mzinda wa Yehova, Ziyoni+ wa Woyera wa Isiraeli.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena