Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 23:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Inetu ndalamulidwa kudzadalitsa,

      Ndipo Iye wadalitsa,+ ine sindisintha zimenezo.+

  • 1 Mbiri 28:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Tsopano mwaima pamaso pa Aisiraeli onse, amene ndi mpingo wa Yehova,+ ndiponso Mulungu wathu akumva zimenezi.+ Choncho samalani ndi kutsatira malamulo onse a Yehova Mulungu wanu, kuti dziko labwinoli+ likhale lanu ndi kuti mudzasiyire ana anu obwera pambuyo panu monga cholowa chawo mpaka kalekale.

  • 1 Timoteyo 4:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Pakuti kuchita masewera olimbitsa thupi n’kopindulitsa pang’ono, koma kukhala wodzipereka kwa Mulungu+ n’kopindulitsa m’zonse,+ chifukwa kumakhudza lonjezo la moyo uno ndi moyo umene ukubwerawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena