Salimo 111:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndi ochirikizika bwino mpaka muyaya, ndithu mpaka kalekale,+ע [ʽAʹyin]Ndipo amawapereka m’choonadi ndiponso molungama.+ Salimo 119:137 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 137 Ndinu wolungama inu Yehova,+Ndipo zigamulo zanu ndi zowongoka.+ Miyambo 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mvetserani chifukwa ndikulankhula zinthu zofunika kwambiri.+ Ndikutsegula pakamwa panga kuti ndinene zowongoka.+
8 Ndi ochirikizika bwino mpaka muyaya, ndithu mpaka kalekale,+ע [ʽAʹyin]Ndipo amawapereka m’choonadi ndiponso molungama.+
6 Mvetserani chifukwa ndikulankhula zinthu zofunika kwambiri.+ Ndikutsegula pakamwa panga kuti ndinene zowongoka.+